Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, anadza amuna asanu ndi mmodzi, odzera njira ya cipata ca kumtunda coloza kumpoto, ali yense ndi cida cace cophera m'dzanja lace; ndi munthu mmodzi pakati pao wobvala bafuta, ndi zolembera nazo m'cuuno mwace. Ndipo analowa, naima m'mphepete mwa guwa la nsembe lamkuwa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 9

Onani Ezekieli 9:2 nkhani