Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali caka cacisanu ndi cimodzi, mwezi wacisanu ndi cimodzi, tsiku lacisanu la mweziwo, pokhala ine m'nyumba mwanga, akulu a Yuda omwe analikukhala pamaso panga, dzanja la Yehova Mulungu linandigwera komweko.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 8

Onani Ezekieli 8:1 nkhani