Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 7:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cokometsera cace cokongola anaciyesa codzikuza naco, napanga naco mafanizo ao onyansa, ndi zonyansa zao zina; cifukwa cace ndinapatsa ici cikhale cowadetsa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:20 nkhani