Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 7:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti wogulitsa sadzabwera ku cogulitsaco, cinkana akali ndi moyo, popeza masomphenyawo akunena unyinji wace wonse sadzapita pacabe, ndipo palibe mmodzi adzalimbitsa moyo wace m'mphulupulu yace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:13 nkhani