Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 6:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nunene, Mapiri a Israyeli inu, tamverani mau a Yehova Mulungu: Atero Yehova Mulungu kwa mapiri ndi zitunda, kwa mitsinje ndi zigwa, Taonani, Ine ndikufikitsirani lupanga, ndipo ndidzaononga misanje yanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 6

Onani Ezekieli 6:3 nkhani