Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 6:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova Mulungu, Omba manja ako, ponda ndi phazi lako, nuti, Kalanga ine, cifukwa ca zonyansa zoipa zonse za nyumba ya Israyeli; pakuti adzagwa ndi lupanga, ndi njala, ndi mliri.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 6

Onani Ezekieli 6:11 nkhani