Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuwatumizira Ine mibvi yoipa ya njala yakuononga, imene ndidzatumiza kukuonongani, pamenepo ndidzakukuzirani njala, ndi kukutyolerani mcirikizo, ndiwo cakudya.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:16 nkhani