Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 48:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo madera otsalawo m'litali mwace alingane ndi copereka copatulika, ndico zikwi khumi kum'mawa, ndi zikwi khumi kumadzulo, alingane ndi copereka copatulika; ndi zipatso zace zikhale za cakudya ca iwo ogwira nchito m'mudzi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48

Onani Ezekieli 48:18 nkhani