Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 48:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi miyeso yace ndi iyi: mbali ya kumpoto, mabango zikwi zinai mphambu mazana asanu; ndi mbali ya kumwela, zikwi zinai mphambu mazana asanu; ndi mbali ya kummawa, zikwi zinai mphambu mazana asanu; ndi mbali ya kumadzulo, zikwi zinai mphambu mazana asanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48

Onani Ezekieli 48:16 nkhani