Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 48:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo asagulitseko, kapena kulisintha, kapena kupitiriza zipatso zoyamba za dziko; pakuti liri lopatulika la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48

Onani Ezekieli 48:14 nkhani