Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 47:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzakhala nalo colowa canu wina ndi mnzace yemwe, ndilo limene ndinakwezapo dzanja langa kulipereka kwa makolo anu, ndi dziko ili lidzakugwerani colowa canu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:14 nkhani