Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 47:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kumtsinje, kugombe kwace tsidya lino ndi lija, kudzamera mtengo uli wonse wa cakudya, osafota tsamba lace, zipatso zace zomwe zosasowa; idzabala zipatso zatsopano mwezi ndi mwezi, popeza madzi ace atumphuka m'malo opatulika; ndi zipatso zace zidzakhala cakudya, ndi tsamba lace lakuciritsa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:12 nkhani