Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 46:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pofika anthu a m'dziko pamaso pa Yehova m'madyerero oikika, iye amene alowera njira ya ku cipata ca kumpoto kudzalambira, aturukire njira ya ku cipata ca kumwera; ndi iye amene alowera njira ya ku cipata ca kumwera, aturukire njira ya ku cipata ca kumpoto; asabwerere njira ya cipata anadzeraco, koma aturukire m'tsogolo mwace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:9 nkhani