Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 46:23-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Ndipo panali maguwa pozungulira pace m'menemo, pozungulira pace pa mabwalo anai; ndipo anamanga maguwawo ndi mafuwa pansi pace pozungulirapo.

24. Ndipo anati kwa ine, Izi ndi nyumba zophikiramo, kumene atumiki a kacisi aziphikira nsembe ya anthu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46