Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 46:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kalonga asatengeko colowa ca anthu kuwazunza, ndi kulanda dziko lao lao; apatse ana ace colowa kulemba dziko lace lace, kuti anthu anga asabalalike, yense kucoka m'dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:18 nkhani