Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Ambuye Yehova, Likufikireni akalonga a Israyeli inu, lekani kucita ciwawa, ndi kulanda za eni ace; mucite ciweruzo ndi cilungamo; lekani kupitikitsa anthu anga m'zolowa zao, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:9 nkhani