Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwezi wacisanu ndi ciwiri, tsiku lakhumi ndi cisanu la mwezi, pamadyerero, acite momwemo masiku asanu ndi awiri, monga mwa nsembe yaucimo, monga mwa nsembe yopsereza, ndi monga mwa nsembe yaufa, ndi monga mwa mafuta.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:25 nkhani