Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo masiku asanu ndi awiri a madyerero akonzere Yehova nsembe yopsereza, ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri zopanda cirema, tsiku ndi tsiku, masiku asanu ndi awiriwa; ndi tonde tsiku ndi tsiku, akhale wa nsembe yaucimo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:23 nkhani