Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo udindo wa kalonga ndiwo kupereka nsembe zopsereza, ndi nsembe zaufa, ndi nsembe zothira, pamadyerero, ndi pokhala mwezi, ndi pamasabata; pa madyerero onse oikika a nyumba ya Israyeli; ndipo apereke nsembe yaucimo, ndi nsembe yaufa, ndi nsembe yopsereza, ndi nsembe zamtendere, kucitira cotetezera nyumba ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:17 nkhani