Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Copereka mucipereke ndico limodzi la magawo asanu ndi limodzi la efa, kulitapa pa homeri wa tirigu; muperekenso limodzi la magawo asanu ndi limodzi la efa, kulitapa pa homeri wa barele;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:13 nkhani