Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 44:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Cipata ici citsekeke, cisatseguke, osalowako munthu; pakuti Yehova Mulungu wa Israyeli walowerapo; cifukwa cace citsekeke.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:2 nkhani