Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 43:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku laciwiri upereke tonde wopanda cirema, akhale nsembe yaucimo; ndipo ayeretse guwa la nsembe monga umo analiyeretsera ndi ng'ombeyo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:22 nkhani