Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 43:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, atero Ambuye Yehova, Malemba a guwa la nsembe, tsiku lakulimanga, kuperekapo nsembe zopsereza, ndi kuwazapo mwazi, ndi awa;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:18 nkhani