Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 42:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zipinda zapamwamba zinacepa, pakuti makonde am'mwamba analanda pamenepo, cifukwa cace zinacepa koposa zapansi ndi zapakati m'nyumba yazipinda.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:5 nkhani