Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 42:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo njira ya pakhomo pao inanga maonekedwe a njira ya ku nyumba yazipinda yoloza kumpoto, inalingana nayo m'litali mwace, momwemonso kupingasa kwace; ndi m'maturukiro mwace monse munali monga mwa macitidwe a inzace, ndi monga mwa makomo a inzace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:11 nkhani