Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 41:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zipinda za m'mphepete zinakula m'kupingasa kwao, pozinga nyumba m'kukwera kwao; pakuti nyumba inazingika mokwerakwera pozungulira pace pa nyumba; motero kupingasa kwace kwa nyumba kunakula kumwamba kwace, momwemonso anakwera kuyambira cipinda cakunsi, kupita capakati, kufikira cam'mwamba.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:7 nkhani