Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 40:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anafika ku cipata coloza kum'mawa, nakwera pa makwerero ace; ndipo anayesa ciundo ca cipata, bango limodzi kucindikira kwace; ndico ciundo coyamba, bango limodzi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:6 nkhani