Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 40:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali magome anai a nsembe yopsereza a miyala yosema, m'litali mwace mkono ndi nusu, kupingasa kwace mkono ndi nusu, msinkhu wace mkono umodzi; pamenepo adafoika zipangizo zimene anaphera nazo nsembe yopsereza ndi nsembe yophera.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:42 nkhani