Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 40:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ku mbali yina ya khonde kunja, pakukwerera polowera pa cipata ca kumpoto, kunali magome awiri, ndi ku mbali inzace ya kucipata kunali magome awiri.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:40 nkhani