Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 40:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zidundumwa zace zinaloza ku bwalo lakunja; ndi pa nsanamira zace panali akanjedza cakuno ndi cauko; ndipo pokwerera pace panali makwerero asanu ndi atatu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:34 nkhani