Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 40:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali cipata ca bwalo lam'kati, copenyana ndi cipata cinzace cakunja kumpoto, ndi ca kum'mawa; ndipo anayesa kuyambira kucipata kufikira kucipata mikono zana.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:23 nkhani