Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 40:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali mazenera a made okhazikika pazipinda ndi m'makhoma a pakati pao, m'kati mwa cipata pozungulira ponse; momwemonso pazidundumwa; ndipo panali mazenera pozungulira ponse m'katimo, pa nsanamirazo panali akanjedza.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:16 nkhani