Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 39:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo okhala m'midzi ya Israyeli adzaturuka, nadzasonkha moto, nadzatentha zida za nkhondo, ndi zikopa zocinjiriza, mauta, ndi mibvi, ndi ndodo, ndi mikondo; ndipo adzasonkha moto nazo zaka zisanu ndi ziwiri;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:9 nkhani