Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 39:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudzadya nyama ya amphamvu, ndi kumwa mwazi wa akalonga a padziko, wa nkhosa zamphongo, wa ana a nkhosa, ndi wa mbuzi, ndi wa ng'ombe, zonsezi zonenepa za ku Basana.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:18 nkhani