Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 39:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika tsiku ilo, ndidzapatsa Gogi manda m'Israyeli, cigwa ca opitawo kum'mawa kwa nyanja; ndipo lidzaletsa opitawo, ndipo adzaika komweko Gogi ndi unyinji wace wonse, nadzacicha, Cigwa ca unyinji wa Gogi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:11 nkhani