Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 39:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, nenera motsutsana naye Gogi, uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe Gogi, iwe mfumu yaikuru ya Meseki ndi Tubala;

2. ndipo ndidzakutembenuza, ndi kukutsogolera, ndi kukweza iwe ucoke ku malekezero a kumpoto; ndipo ndidzadza nawe ku mapiri a Israyeli;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39