Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 38:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalimbana naye ndi mliri ndi mwazi; ndipo ndidzambvumbitsira iye, ndi magulu ace, ndi mitundu yambiri ya anthu okhala naye mbvumbi waukuru, ndi matalala akuru, moto ndi sulfure.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 38

Onani Ezekieli 38:22 nkhani