Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 38:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

motero kuti nsomba za m'nyanja, ndi mbalame za m'mlengalenga, ndi nyama za kuthengo, ndi zokwawa zonse zakukwawa pansi, ndi anthu onse akukhala padziko, zidzanjenjemera pamaso panga; ndi mapiri adzagwetsedwa, ndi potsetsereka padzagumuka, ndi makoma onse adzagwa pansi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 38

Onani Ezekieli 38:20 nkhani