Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 37:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono, iwe wobadwa ndi munthu, Tenga mtengo umodzi, nulembepo, Wa Yuda ndi wa ana a Israyeli anzace; nutenge mtengo wina, nulembepo, Wa Yosefe, mtengo wa Efraimu, ndi wa nyumba yonse ya Israyeli anzace;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:16 nkhani