Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 36:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace, mapiri inu a Israyeli, imvani mau a Ambuye Yehova. Atero Ambuye Yehova kunena ndi mapiri, ndi zitunda, ndi mitsinje, ndi zigwa, ndi zipululu zopasuka, ndi midzi yamabwinja, imene yakhala cakudya ndi coseketsa amitundu otsala akuzungulira;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:4 nkhani