Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 36:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzazindikiritsa dzina langa lalikuru kuti liri loyera, limene laipitsidwa mwa amitundu, limene inu munaliipsa pakati pao; ndipo amitundu adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, ati Ambuye Yehova, pozindikiridwa Ine woyera mwa inu pamaso pao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:23 nkhani