Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 36:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakucurukitsirani anthu ndi nyama; ndipo adzacuruka, nadzabalana; ndipo ndidzakhalitsa anthu pa inu, monga umo anakhalira kale, ndipo ndidzacitira inu zabwino koposa poyamba paja; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:11 nkhani