Ndipo ndidzadzaza mapiri ace ndi ophedwa ace pa zitunda zako, ndi m'zigwa zako, ndi m'mitsinje mwako monse; adzagwa ophedwa ndi lupanga.