Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 35:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga momwe unakondwerera colowa ca nyumba ya Israyeli, papeza cidapasuka, momwemo ndidzakucitira iwe; udzakhala wopasuka, phiri la Seiri iwe, ndi Edomu lonse lonseli; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 35

Onani Ezekieli 35:15 nkhani