Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 34:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pali ine, ati Ambuye Yehova, zedi, popeza nkhosa zanga zinakhala nyama, ndi nkhosa zanga zinakhala cakudya ca zirombo zonse za kuthengo, cifukwa kunalibe mbusa, ndi abusa anga sanafunafuna nkhosa zanga, koma abusawo anadzidyetsa okha, osadyetsa nkhosa zanga;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:8 nkhani