Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 34:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzapangana nazo pangano la mtendere, ndi kuleketsa zirombo zoipa m'dzikomo; ndipo zidzakhala mosatekeseka m'cipululu, ndi kugona kunkhalango.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:25 nkhani