Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 34:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzazidyetsa podyetsa pabwino; ndi pa mapiri atali a Israyeli padzakhala kholo lao, apo adzagona m'khola mwabwino, nadzadya podyetsa pokometsetsa pa mapiri a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:14 nkhani