Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 33:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma dzanja la Yehova linandikhalira madzulo, asanandifike wopulumukayo; ndipo ananditsegula pakamwa mpaka anandifika m'mawa, m'mwemo panatseguka pakamwa panga, wosakhalanso wosalankhula.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:22 nkhani