Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 31:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndirtagwedeza amitundu ndi phokoso la kugwa kwace, muja ndinamgwetsera kumanda, pamodzi ndi iwo otsikira kumanda; ndi mitengo yonse ya ku Edene yosankhika, ndi yokometsetsa ya ku Lebano, yonse yakumwa madzi, inasangalala munsi mwace mwa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 31

Onani Ezekieli 31:16 nkhani