Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 31:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo alendo oopsawo a amitundu anaulikhatu, nausiya; nthawi zace zidagwa pamapiri ndi m'zigwa zonse, ndi nthambi zace zinatyokera ku timitsinje tonse ta m'dziko; ndi mitundu yonse ya anthu a pa dziko lapansi inatsika ku mthunzi wace, niusiya.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 31

Onani Ezekieli 31:12 nkhani